Mlaliki 2:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Munthu wanzeru maso ake amaona bwino+ koma wopusa amayenda mumdima.+ Komanso ndazindikira kuti zimene zimachitikira onsewa nʼzofanana.+
14 Munthu wanzeru maso ake amaona bwino+ koma wopusa amayenda mumdima.+ Komanso ndazindikira kuti zimene zimachitikira onsewa nʼzofanana.+