Mlaliki 2:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Choncho mumtima mwanga ndinanena kuti: “Zimene zimachitikira opusa inenso zidzandichitikira.”+ Ndiye ndinapindula chiyani chifukwa chokhala wanzeru kwambiri? Choncho mumtima mwanga ndinanena kuti: “Izinso nʼzachabechabe.”
15 Choncho mumtima mwanga ndinanena kuti: “Zimene zimachitikira opusa inenso zidzandichitikira.”+ Ndiye ndinapindula chiyani chifukwa chokhala wanzeru kwambiri? Choncho mumtima mwanga ndinanena kuti: “Izinso nʼzachabechabe.”