Mlaliki 2:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Choncho ndinayamba kudana ndi moyo+ chifukwa ndinkaona kuti chilichonse chimene chikuchitika padziko lapansi pano chikupangitsa kuti ndizivutika mumtima. Chifukwa zonse zinali zachabechabe,+ zinali ngati kuthamangitsa mphepo.+
17 Choncho ndinayamba kudana ndi moyo+ chifukwa ndinkaona kuti chilichonse chimene chikuchitika padziko lapansi pano chikupangitsa kuti ndizivutika mumtima. Chifukwa zonse zinali zachabechabe,+ zinali ngati kuthamangitsa mphepo.+