21 Chifukwa munthu akhoza kugwira ntchito mwakhama ndipo angachite zonse mwanzeru, mozindikira komanso mwaluso. Koma amayenerabe kupereka zonse zimene ali nazo kwa munthu amene sanagwire ntchito iliyonse kuti apeze zinthuzo.+ Zimenezinso nʼzachabechabe ndipo nʼzomvetsa chisoni kwambiri.