Mlaliki 2:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Chifukwa masiku onse a moyo wake, ntchito yakeyo imamubweretsera zowawa ndi zokhumudwitsa.+ Ndipo ngakhale usiku mtima wake supuma.+ Izinso nʼzachabechabe.
23 Chifukwa masiku onse a moyo wake, ntchito yakeyo imamubweretsera zowawa ndi zokhumudwitsa.+ Ndipo ngakhale usiku mtima wake supuma.+ Izinso nʼzachabechabe.