Mlaliki 2:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Palibe chabwino kwa munthu kuposa kuti adye, amwe ndi kusangalala chifukwa choti wagwira ntchito mwakhama.+ Ndinazindikira kuti zimenezinso nʼzochokera mʼdzanja la Mulungu woona,+ Mlaliki Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:24 Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 37 Galamukani!,10/2014, tsa. 61/8/1998, tsa. 11 Nsanja ya Olonda,7/1/2011, tsa. 7
24 Palibe chabwino kwa munthu kuposa kuti adye, amwe ndi kusangalala chifukwa choti wagwira ntchito mwakhama.+ Ndinazindikira kuti zimenezinso nʼzochokera mʼdzanja la Mulungu woona,+
2:24 Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 37 Galamukani!,10/2014, tsa. 61/8/1998, tsa. 11 Nsanja ya Olonda,7/1/2011, tsa. 7