Mlaliki 3:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 komanso kuti munthu aliyense adye ndi kumwa nʼkumasangalala ndi zinthu zabwino, chifukwa cha ntchito yake yonse imene waigwira mwakhama. Imeneyi ndi mphatso yochokera kwa Mulungu.+ Mlaliki Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:13 Nsanja ya Olonda,12/15/2009, tsa. 193/1/2006, tsa. 172/15/1997, ptsa. 16-177/15/1989, ptsa. 4-7
13 komanso kuti munthu aliyense adye ndi kumwa nʼkumasangalala ndi zinthu zabwino, chifukwa cha ntchito yake yonse imene waigwira mwakhama. Imeneyi ndi mphatso yochokera kwa Mulungu.+