Mlaliki 3:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndazindikira kuti zonse zimene Mulungu woona amapanga zidzakhalapo mpaka kalekale. Palibe choti nʼkuwonjezerapo kapena kuchotsapo. Mulungu woona anazipanga mwanjira imeneyi kuti anthu azimuopa.+
14 Ndazindikira kuti zonse zimene Mulungu woona amapanga zidzakhalapo mpaka kalekale. Palibe choti nʼkuwonjezerapo kapena kuchotsapo. Mulungu woona anazipanga mwanjira imeneyi kuti anthu azimuopa.+