Mlaliki 3:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Chilichonse chimene chikuchitika chinachitikapo kale ndipo zimene zidzachitike zinachitikapo kale.+ Koma Mulungu woona amafufuza zinthu zimene anthu akuzifunafuna.* Mlaliki Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:15 Nsanja ya Olonda,11/1/2006, tsa. 14
15 Chilichonse chimene chikuchitika chinachitikapo kale ndipo zimene zidzachitike zinachitikapo kale.+ Koma Mulungu woona amafufuza zinthu zimene anthu akuzifunafuna.*