Mlaliki 3:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ine ndaonanso zinthu izi padziko lapansi pano: Pamene panayenera kukhala chilungamo panali zoipa, ndipo pamene panayenera kuchitika zachilungamo panachitika zoipa.+
16 Ine ndaonanso zinthu izi padziko lapansi pano: Pamene panayenera kukhala chilungamo panali zoipa, ndipo pamene panayenera kuchitika zachilungamo panachitika zoipa.+