Mlaliki 3:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Choncho mumtima mwanga ndinanena kuti: “Mulungu woona adzaweruza olungama ndi oipa omwe+ chifukwa pali nthawi yoyenera yoti chinthu chilichonse chichitike.” Mlaliki Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:17 Nsanja ya Olonda,10/1/1999, tsa. 14
17 Choncho mumtima mwanga ndinanena kuti: “Mulungu woona adzaweruza olungama ndi oipa omwe+ chifukwa pali nthawi yoyenera yoti chinthu chilichonse chichitike.”