Mlaliki 3:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Chifukwa anthu ali ndi mapeto ndipo nyamanso zili ndi mapeto. Mapeto a zonsezi ndi ofanana.+ Nyama imafa ndipo munthunso amafa, zonsezi zili ndi mzimu wofanana.+ Choncho munthu saposa nyama, chifukwa zinthu zonse nʼzachabechabe. Mlaliki Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:19 Nsanja ya Olonda,2/15/1997, ptsa. 10-11 Kukambitsirana, tsa. 322
19 Chifukwa anthu ali ndi mapeto ndipo nyamanso zili ndi mapeto. Mapeto a zonsezi ndi ofanana.+ Nyama imafa ndipo munthunso amafa, zonsezi zili ndi mzimu wofanana.+ Choncho munthu saposa nyama, chifukwa zinthu zonse nʼzachabechabe.