Mlaliki 4:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Awiri amaposa mmodzi+ chifukwa amapeza mphoto yabwino* pa ntchito yawo imene amaigwira mwakhama. Mlaliki Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:9 Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 42