Mlaliki 5:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Uzisamala mmene ukuyendera ukapita kunyumba ya Mulungu woona.+ Ndi bwino kuti ukapita kumeneko uzikamvetsera,+ kusiyana ndi kukapereka nsembe ngati mmene anthu opusa amachitira+ chifukwa iwo sakudziwa kuti zimene akuchita nʼzoipa.
5 Uzisamala mmene ukuyendera ukapita kunyumba ya Mulungu woona.+ Ndi bwino kuti ukapita kumeneko uzikamvetsera,+ kusiyana ndi kukapereka nsembe ngati mmene anthu opusa amachitira+ chifukwa iwo sakudziwa kuti zimene akuchita nʼzoipa.