Mlaliki 5:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Maloto amabwera chifukwa chochuluka zochita,*+ ndipo munthu wopusa akamalankhula zinthu zambiri, zimachititsa kuti alankhule zinthu zopanda pake.+ Mlaliki Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:3 Nsanja ya Olonda,11/1/2006, tsa. 15 Galamukani!,8/8/1994, tsa. 24
3 Maloto amabwera chifukwa chochuluka zochita,*+ ndipo munthu wopusa akamalankhula zinthu zambiri, zimachititsa kuti alankhule zinthu zopanda pake.+