Mlaliki 5:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Zinthu zabwino zikachuluka ozidya amachulukanso.+ Ndipo kodi mwiniwake wa zinthuzo amapindula chiyani kuposa kumangoziyangʼana ndi maso ake?+ Mlaliki Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:11 Nsanja ya Olonda,5/15/1998, ptsa. 4-5
11 Zinthu zabwino zikachuluka ozidya amachulukanso.+ Ndipo kodi mwiniwake wa zinthuzo amapindula chiyani kuposa kumangoziyangʼana ndi maso ake?+