Mlaliki 6:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Chilichonse chimene chinakhalapo chinapatsidwa kale dzina ndipo nʼzodziwika kuti munthu ndi ndani. Iye sangathe kutsutsana* ndi amene ali wamphamvu kuposa iyeyo.
10 Chilichonse chimene chinakhalapo chinapatsidwa kale dzina ndipo nʼzodziwika kuti munthu ndi ndani. Iye sangathe kutsutsana* ndi amene ali wamphamvu kuposa iyeyo.