Mlaliki 7:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndi bwino kupita kunyumba yamaliro kusiyana ndi kupita kunyumba yamadyerero,+ chifukwa amenewo ndi mapeto a munthu aliyense, ndipo amene ali ndi moyo aziganizira zimenezi mumtima mwake. Mlaliki Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 7:2 Galamukani!,4/8/2003, tsa. 319/8/1994, ptsa. 28-29 Nsanja ya Olonda,6/1/2002, tsa. 410/15/1990, tsa. 31
2 Ndi bwino kupita kunyumba yamaliro kusiyana ndi kupita kunyumba yamadyerero,+ chifukwa amenewo ndi mapeto a munthu aliyense, ndipo amene ali ndi moyo aziganizira zimenezi mumtima mwake.
7:2 Galamukani!,4/8/2003, tsa. 319/8/1994, ptsa. 28-29 Nsanja ya Olonda,6/1/2002, tsa. 410/15/1990, tsa. 31