Mlaliki 7:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Munthu wanzeru amene ali mʼnyumba yamaliro, amaganizira mozama za moyo ndi imfa. Koma munthu wopusa, nthawi zonse amaganizira za zisangalalo.+ Mlaliki Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 7:4 Nsanja ya Olonda,4/15/2008, tsa. 22
4 Munthu wanzeru amene ali mʼnyumba yamaliro, amaganizira mozama za moyo ndi imfa. Koma munthu wopusa, nthawi zonse amaganizira za zisangalalo.+