Mlaliki 7:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Kuseka kwa anthu opusa kuli ngati kuthetheka kwa minga zomwe zikuyaka pansi pa mphika.+ Zimenezinso nʼzachabechabe. Mlaliki Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 7:6 Nsanja ya Olonda,11/1/2006, tsa. 153/15/1996, tsa. 4
6 Kuseka kwa anthu opusa kuli ngati kuthetheka kwa minga zomwe zikuyaka pansi pa mphika.+ Zimenezinso nʼzachabechabe.