Mlaliki 7:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Koma kuponderezedwa kungapangitse munthu wanzeru kuchita zinthu ngati wamisala, ndipo chiphuphu chimawononga mtima wa munthu.+ Mlaliki Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 7:7 Nsanja ya Olonda,9/1/2010, tsa. 47/1/1992, tsa. 4
7 Koma kuponderezedwa kungapangitse munthu wanzeru kuchita zinthu ngati wamisala, ndipo chiphuphu chimawononga mtima wa munthu.+