Mlaliki 7:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Mapeto a chinthu amakhala bwino kuposa chiyambi chake. Ndipo kukhala woleza mtima ndi kwabwino kuposa kukhala wodzikuza.+ Mlaliki Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 7:8 Nsanja ya Olonda,9/1/2000, tsa. 46/15/1995, ptsa. 10-11
8 Mapeto a chinthu amakhala bwino kuposa chiyambi chake. Ndipo kukhala woleza mtima ndi kwabwino kuposa kukhala wodzikuza.+