Mlaliki 7:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Pa tsiku labwino, uzichitanso zinthu zabwino.+ Koma pa tsiku latsoka uzikumbukira kuti Mulungu woona anapanga masiku onsewa+ nʼcholinga choti anthu asamadziwe chilichonse chimene chidzawachitikire mʼtsogolo.+ Mlaliki Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 7:14 Nsanja ya Olonda,5/1/1999, tsa. 29
14 Pa tsiku labwino, uzichitanso zinthu zabwino.+ Koma pa tsiku latsoka uzikumbukira kuti Mulungu woona anapanga masiku onsewa+ nʼcholinga choti anthu asamadziwe chilichonse chimene chidzawachitikire mʼtsogolo.+