Mlaliki 7:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndi bwino kwambiri kuti usunge malangizo onsewa, usasiyepo ena.+ Chifukwa munthu amene amaopa Mulungu adzamvera malangizo onsewa.
18 Ndi bwino kwambiri kuti usunge malangizo onsewa, usasiyepo ena.+ Chifukwa munthu amene amaopa Mulungu adzamvera malangizo onsewa.