-
Mlaliki 7:23Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
23 Ndinaganizira zinthu zonsezi mwanzeru ndipo ndinati: “Ndidzakhala wanzeru.” Koma zinali zosatheka kuti ndipeze nzeruzo.
-