Mlaliki 7:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Zimene ndapeza ndi izi zokha: Mulungu woona anapanga anthu owongoka mtima,+ koma anthuwo asankha kuchita zinthu zogwirizana ndi zolinga zawo.”+ Mlaliki Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 7:29 Nsanja ya Olonda,5/1/1999, ptsa. 28-29
29 Zimene ndapeza ndi izi zokha: Mulungu woona anapanga anthu owongoka mtima,+ koma anthuwo asankha kuchita zinthu zogwirizana ndi zolinga zawo.”+