Mlaliki 8:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndi ndani angafanane ndi munthu wanzeru? Ndipo ndi ndani akudziwa njira yothetsera vuto?* Nzeru za munthu zimachititsa nkhope yake kuwala ndipo nkhope yake yokwiya imasintha nʼkumaoneka bwino.
8 Ndi ndani angafanane ndi munthu wanzeru? Ndipo ndi ndani akudziwa njira yothetsera vuto?* Nzeru za munthu zimachititsa nkhope yake kuwala ndipo nkhope yake yokwiya imasintha nʼkumaoneka bwino.