Mlaliki 8:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Usafulumire kuchoka pamaso pake,+ ndipo usayambe kuchita nawo zinthu zoipa.+ Chifukwa mfumuyo ikhoza kuchita chilichonse chimene ikufuna kuchita, Mlaliki Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:3 Nsanja ya Olonda,11/1/2006, tsa. 16
3 Usafulumire kuchoka pamaso pake,+ ndipo usayambe kuchita nawo zinthu zoipa.+ Chifukwa mfumuyo ikhoza kuchita chilichonse chimene ikufuna kuchita,