Mlaliki 8:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndaona anthu oipa akuikidwa mʼmanda, amene ankalowa ndi kutuluka mʼmalo oyera, koma sanachedwe kuiwalika mumzinda umene ankachitiramo zinthu zoipa.+ Izinso nʼzachabechabe.
10 Ndaona anthu oipa akuikidwa mʼmanda, amene ankalowa ndi kutuluka mʼmalo oyera, koma sanachedwe kuiwalika mumzinda umene ankachitiramo zinthu zoipa.+ Izinso nʼzachabechabe.