Mlaliki 8:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ndinatsimikiza mumtima mwanga kuti ndipeze nzeru ndiponso kuti ndione zinthu zonse* zimene zikuchitika padziko lapansi,+ mpaka kufika pomasala tulo masana ndi usiku.* Mlaliki Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:16 Nsanja ya Olonda,11/1/2006, tsa. 16
16 Ndinatsimikiza mumtima mwanga kuti ndipeze nzeru ndiponso kuti ndione zinthu zonse* zimene zikuchitika padziko lapansi,+ mpaka kufika pomasala tulo masana ndi usiku.*