Mlaliki 9:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Chilichonse chimene dzanja lako lapeza kuti lichite, uchichite ndi mphamvu zako zonse, chifukwa ku Manda*+ kumene ukupitako kulibe kugwira ntchito, kuganiza zochita, kudziwa zinthu kapena nzeru. Mlaliki Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9:10 Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 29 Nsanja ya Olonda,12/15/2015, tsa. 116/15/2006, tsa. 5
10 Chilichonse chimene dzanja lako lapeza kuti lichite, uchichite ndi mphamvu zako zonse, chifukwa ku Manda*+ kumene ukupitako kulibe kugwira ntchito, kuganiza zochita, kudziwa zinthu kapena nzeru.
9:10 Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 29 Nsanja ya Olonda,12/15/2015, tsa. 116/15/2006, tsa. 5