Mlaliki 9:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Chifukwa munthu sadziwa nthawi imene tsoka lingamugwere.+ Mofanana ndi nsomba zimene zimagwidwa mu ukonde wakupha, komanso mbalame zimene zimagwidwa mumsampha, ana a anthu nawonso amakodwa pa nthawi yatsoka, tsokalo likawagwera mwadzidzidzi. Mlaliki Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9:12 Nsanja ya Olonda,11/1/2005, ptsa. 3-4
12 Chifukwa munthu sadziwa nthawi imene tsoka lingamugwere.+ Mofanana ndi nsomba zimene zimagwidwa mu ukonde wakupha, komanso mbalame zimene zimagwidwa mumsampha, ana a anthu nawonso amakodwa pa nthawi yatsoka, tsokalo likawagwera mwadzidzidzi.