-
Mlaliki 9:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Panali mzinda winawake waungʼono ndipo munali amuna ochepa. Kenako kunabwera mfumu yamphamvu ndipo inazungulira mzindawo nʼkuunjika milu ikuluikulu yadothi yoti imenyerepo nkhondo.
-