Mlaliki 9:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Mumzindawo munali munthu wosauka koma wanzeru ndipo anapulumutsa mzindawo chifukwa cha nzeru zakezo. Koma palibe aliyense amene anakumbukira munthu wosaukayo.+
15 Mumzindawo munali munthu wosauka koma wanzeru ndipo anapulumutsa mzindawo chifukwa cha nzeru zakezo. Koma palibe aliyense amene anakumbukira munthu wosaukayo.+