Mlaliki 9:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Choncho ndinaganiza kuti: ‘Nzeru nʼzabwino kuposa mphamvu,+ koma anthu amanyoza nzeru za munthu wosauka ndipo samvera mawu ake.’+ Mlaliki Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9:16 Nsanja ya Olonda,8/1/2000, tsa. 32
16 Choncho ndinaganiza kuti: ‘Nzeru nʼzabwino kuposa mphamvu,+ koma anthu amanyoza nzeru za munthu wosauka ndipo samvera mawu ake.’+