Mlaliki 10:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mʼnjira iliyonse imene munthu wopusa amayenda, amachita zinthu mopanda nzeru,*+ ndipo amaonetsetsa kuti aliyense adziwe kuti iye ndi wopusa.+
3 Mʼnjira iliyonse imene munthu wopusa amayenda, amachita zinthu mopanda nzeru,*+ ndipo amaonetsetsa kuti aliyense adziwe kuti iye ndi wopusa.+