-
Mlaliki 10:10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Ngati nkhwangwa yabunthwa ndipo munthu sanainole, adzafunika kugwiritsa ntchito mphamvu zambiri. Koma nzeru zimathandiza kuti zinthu ziyende bwino.
-