Mlaliki 10:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ngakhale zili choncho, munthu wopusa amangolankhulabe.+ Munthu sadziwa chimene chidzachitike. Ndi ndani amene angamuuze zimene zidzachitike iye atafa?+
14 Ngakhale zili choncho, munthu wopusa amangolankhulabe.+ Munthu sadziwa chimene chidzachitike. Ndi ndani amene angamuuze zimene zidzachitike iye atafa?+