Mlaliki 10:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Zimakhala zosangalatsa ngati mfumu imene ikulamulira mʼdziko ndi mwana wochokera kubanja lachifumu ndipo akalonga amadya pa nthawi yake kuti apeze mphamvu, osati nʼcholinga choti aledzere.+
17 Zimakhala zosangalatsa ngati mfumu imene ikulamulira mʼdziko ndi mwana wochokera kubanja lachifumu ndipo akalonga amadya pa nthawi yake kuti apeze mphamvu, osati nʼcholinga choti aledzere.+