Mlaliki 12:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Uchite zimenezi kuwala kwa dzuwa, mwezi ndi nyenyezi kusanazime+ ndiponso mitambo yamvula isanabwererenso pambuyo poti mvula yagwa. Mlaliki Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 12:2 Nsanja ya Olonda,11/15/1999, ptsa. 14-15
2 Uchite zimenezi kuwala kwa dzuwa, mwezi ndi nyenyezi kusanazime+ ndiponso mitambo yamvula isanabwererenso pambuyo poti mvula yagwa.