Mlaliki 12:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pa nthawi imeneyo olondera* nyumba adzayamba kunjenjemera, amuna amphamvu adzapindika, akazi adzasiya kupera ufa chifukwa adzatsala ochepa ndipo akazi oyangʼana pawindo azidzaona mdima.+ Mlaliki Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 12:3 Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu,11/2016, tsa. 6 Nsanja ya Olonda,11/15/2008, tsa. 2311/15/1999, tsa. 15
3 Pa nthawi imeneyo olondera* nyumba adzayamba kunjenjemera, amuna amphamvu adzapindika, akazi adzasiya kupera ufa chifukwa adzatsala ochepa ndipo akazi oyangʼana pawindo azidzaona mdima.+
12:3 Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu,11/2016, tsa. 6 Nsanja ya Olonda,11/15/2008, tsa. 2311/15/1999, tsa. 15