-
Mlaliki 12:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Uzikumbukira Mlengi wako chingwe chasiliva chisanachotsedwe, mbale yagolide isanaphwanyidwe, mtsuko umene uli pakasupe usanaphwanyike ndiponso wilo lotungira madzi pachitsime lisanathyoke.
-