Nyimbo ya Solomo 1:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kununkhira kwa mafuta ako ndi kosangalatsa.+ Dzina lako lili ngati mafuta onunkhira amene athiridwa pamutu.+ Nʼchifukwa chake atsikana amakukonda. Nyimbo ya Solomo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:3 Nsanja ya Olonda,1/15/2015, ptsa. 30-3111/15/2006, tsa. 1811/15/1987, tsa. 24
3 Kununkhira kwa mafuta ako ndi kosangalatsa.+ Dzina lako lili ngati mafuta onunkhira amene athiridwa pamutu.+ Nʼchifukwa chake atsikana amakukonda.