Nyimbo ya Solomo 1:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Inu ana aakazi a ku Yerusalemu, ine ndine wakuda koma wokongola,Ngati matenti a ku Kedara+ komanso nsalu za matenti+ a Solomo. Nyimbo ya Solomo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:5 Nsanja ya Olonda,11/15/2006, tsa. 18
5 Inu ana aakazi a ku Yerusalemu, ine ndine wakuda koma wokongola,Ngati matenti a ku Kedara+ komanso nsalu za matenti+ a Solomo.