-
Nyimbo ya Solomo 1:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Musandiyangʼanitsitse chifukwa chakuti ndada,
Ndi dzuwatu landidetsali.
Ana aamuna a mayi anga anandikwiyira.
Choncho anandiika kuti ndiziyangʼanira minda ya mpesa
Moti sindinathe kusamalira munda wanga wa mpesa.
-