-
Nyimbo ya Solomo 3:2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 Choncho ndinati: ‘Ndidzuka nʼkukazungulira mumzinda,
Mʼmisewu ndi mʼmabwalo amumzinda,
Kuti ndikafunefune munthu amene ndimamukonda.’
Ndinamufunafuna koma sindinamupeze.
-