Nyimbo ya Solomo 3:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 “Kodi chinthu chikuchokera kuchipululuchi nʼchiyani, chooneka ngati utsi wokwera mʼmwamba,Chonunkhira mafuta a mule ndi lubani,*Komanso ndi zonunkhira zonse za ufa za munthu wamalonda?”+
6 “Kodi chinthu chikuchokera kuchipululuchi nʼchiyani, chooneka ngati utsi wokwera mʼmwamba,Chonunkhira mafuta a mule ndi lubani,*Komanso ndi zonunkhira zonse za ufa za munthu wamalonda?”+