-
Nyimbo ya Solomo 3:10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Zipilala zake ndi zasiliva,
Motsamira mwake ndi mwagolide.
Chokhalira chake ndi chopangidwa ndi ubweya wa nkhosa wapepo.
Mkati mwake, ana aakazi a ku Yerusalemu
Anakongoletsamo posonyeza chikondi.”
-