-
Nyimbo ya Solomo 5:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Ndakulumbiritsani inu ana aakazi a ku Yerusalemu kuti:
Mukamʼpeza wachikondi wanga,
Mumuuze kuti ine chikondi chikundidwalitsa.”
-