-
Nyimbo ya Solomo 6:1Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 “Kodi wachikondi wako wapita kuti,
Iwe mkazi wokongola kwambiri kuposa akazi onse?
Kodi wachikondi wako wadzera njira iti?
Tiye tikuthandize kumufunafuna.”
-